BAIBO YA DZIKO LATSOPANO

1 Petulo—Za m’Bukuli

Cinyanja
1 Petulo—Za m’Bukuli
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg
nwt 1 Petro

Kalata Yoyamba ya Petulo

Macaputala

1 2 3 4 5

Za m'Bukuli

  • 1

    • Moni (1, 2)

    • Kubadwanso mwatsopano n’kukhala ndi ciyembekezo codalilika (3-12)

    • Khalani oyela monga ana omvela (13-25)

  • 2

    • Muzilakalaka Mau a Mulungu (1-3)

    • Miyala yamoyo yomangidwa m’nyumba yauzimu (4-10)

    • Muzikhala ngati alendo m’dzikoli (11, 12)

    • Kugonjela koyenela (13-25)

      • Khristu ndi citsanzo cathu (21)

  • 3

    • Akazi ndi amuna apabanja (1-7)

    • Muzimvelana cisoni, muziyesetsa kukhala mwamtendele (8-12)

    • Kubvutika cifukwa ca cilungamo (13-22)

      • Muzikhala okonzeka kukhalila kumbuyo ciyembekezo canu (15)

      • Ubatizo ndi cikumbumtima cabwino (21)

  • 4

    • Muzicita cifunilo ca Mulungu, monga anacitila Khristu (1-6)

    • Mapeto a zinthu zonse ali pafupi (7-11)

    • Kubvutika cifukwa cokhala Akhristu (12-19)

  • 5

    • Wetani gulu la nkhosa za Mulungu (1-4)

    • Khalani odzicepetsa komanso khalani maso (5-11)

      • Muzitulila Mulungu nkhawa zanu zonse (7)

      • Mdyelekezi ali ngati mkango wobangula (8)

    • Mau othela (12-14)