BAIBO YA DZIKO LATSOPANO

Tito—Za m’Bukuli

Cinyanja
Tito—Za m’Bukuli
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg
nwt Tito

Kalata kwa Tito

Macaputala

1 2 3

Za m'Bukuli

  • 1

    • Mau oyamba (1-4)

    • Tito aike akulu ku Kerete (5-9)

    • Kudzudzula anthu osalamulilika (10-16)

  • 2

    • Malangizo othandiza kwa acinyamata ndi acikulile (1-15)

      • Kukana umoyo wosaopa Mulungu (12)

      • Kudzipeleka pocita nchito zabwino (14)

  • 3

    • Kugonjela koyenela (1-3)

    • Kukonzekela nchito zabwino (4-8)

    • Kupewa mpatuko komanso kukangana pa zinthu zosathandiza (9-11)

    • Malangizo ena komanso kupeleka moni (12-15)