BAIBO YA DZIKO LATSOPANO

Aefeso—Za m’Bukuli

Cinyanja
Aefeso—Za m’Bukuli
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg
nwt Aefeso

Kalata kwa Aefeso

Macaputala

1 2 3 4 5 6

Za m'Bukuli

  • 1

    • Moni (1, 2)

    • Madalitso auzimu (3-7)

    • Kusonkhanitsa zinthu zonse kwa Khristu (8-14)

      • “Dongosolo” pa nthawi yoikidwilatu (10)

      • Kuikidwa cidindo ndi mzimu woyela monga cikole cotsimikizila (13, 14)

    • Paulo anathokoza Mulungu kaamba ka cikhulupililo ca Aefeso ndipo anawapemphelela (15-23)

  • 2

    • Anapangitsa kuti akhale amoyo mogwilizana ndi Khristu (1-10)

    • Anagwetsa cipupa cimene cinali kuwalekanitsa (11-22)

  • 3

    • Cinsinsi copatulika cinaphatikizapo anthu a mitundu ina (1-13)

      • Anthu a mitundu ina adzalamulila pamodzi ndi Khristu (6)

      • Colinga camuyaya ca Mulungu (11)

    • Apemphelela Aefeso kuti akhale ozindikila (14-21)

  • 4

    • Mgwilizano m’thupi la Khristu (1-16)

      • Mphatso za amuna (8)

    • Umunthu wakale komanso watsopano (17-32)

  • 5

    • Malankhulidwe abwino komanso khalidwe loyela (1-5)

    • Muziyenda ngati ana akuwala (6-14)

    • Dzadzidwani ndi mzimu (15-20)

      • Muziigwilitsa nchito bwino nthawi yanu (16)

    • Malangizo kwa amuna ndi akazi okwatila (21-33)

  • 6

    • Malangizo kwa ana ndi makolo (1-4)

    • Malangizo kwa akapolo ndi ambuye (5-9)

    • Bvalani zida zonse zankhondo zocokela kwa Mulungu (10-20)

    • Moni womaliza (21-24)