Pezani chithunzi choti mudzakambirane monga banja mukamadzaphunzira Baibulo. Koperani ndi kusindikiza chithunzi chilichonse. Ndiyeno malizitsani kujambula chithunzicho polumikiza timadontho kenako n’kuchikongoletsa ndi chekeni. Mukatero, muyankhe mafunso amene ali pachithunzicho.