Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZITHUNZI

Zithunzi

Solomo Anachita Zinthu Mwanzeru

Koperani ndi kusindikiza chithunzichi kuti muphunzire za Mfumu Solomo.

Davide Analimba Mtima Ngakhale Kuti Anali ndi Zida Zochepa

Fananitsani anthu otchulidwa m’Baibulo ndi zinthu zokhudza anthuwo.

Davide Anabwera M’dzina la Mulungu

Thandizani ana anu kuti adziwe zimene dzina la Mulungu limatanthauza.

Kodi Ndi Ndani Amene Anasankha Kutumikira Yehova?

Zochitazi zimathandiza ana a pakati pa zaka 6 ndi 8 kuti adziwe anthu otchulidwa m’Baibulo.