Sankhani anthu otchulidwa m’Baibulo ndiponso mawu amene akufotokoza zimene anthuwo anachita. Sankhaninso anthu amene ankatumikira Mulungu.