Fananitsani anthu otchulidwa m’Baibulo ndi zinthu zokhudza anthuwo zomwe zili m’nkhani ya Davide ndi Goliyati. Kenako mukambirane zimene zinathandiza Davide kuti akhale wolimba mtima.