ZITHUNZI Davide Anabwera M’dzina la Mulungu YAMBANI Ikani zilembo za dzina la Mulungu m’malo ake oyenera ndipo phunzirani tanthauzo la dzinali. Pangani Dawunilodi Nkhani Zina Zithunzi Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi MAKADI A ANTHU OTCHULIDWA M’BAIBULO Khadi la M’Baibulo Lonena za Davide Mwina mukudziwa kale nkhani ya Davide ndi Goliyati, koma pali zambiri zimene mungaphunzire zokhudza Davide. ZITHUNZI Yehova Amaona za Mumtima Koperani chithunzi chokongoletsedwachi ndipo pezani makhalidwe amene angapangitse kuti Mulungu azikukondani. ZOCHITA PA KULAMBIRA KWA PABANJA Kuchita Zinthu Molimba Mtima Phunzitsani ana anu zinthu zimene zimathandiza munthu kuti akhale wolimba mtima. ZITHUNZI ZOFOTOKOZA NKHANI ZA M’BAIBULO Davide Anachita Zinthu Molimba Mtima N’chiyani chinamuchititsa Davide kukhulupirira kuti akhoza kugonjetsa Goliyati? N’chifukwa chiyani inunso muyenera kulimba mtima kuti muchite zinthu zabwino? PHUNZITSANI ANA ANU Davide Sankachita Mantha Werengani nkhaniyi m’Baibulo kuti mudziwe zimene zinamuthandiza Davide kuti akhale wolimba mtima. ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA Zoti Ana Achite Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.