Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Ukhale Wolimba Mtima Ndipo Uchite Zinthu Mwamphamvu

Ukhale Wolimba Mtima Ndipo Uchite Zinthu Mwamphamvu

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. Kusanache,

    Wadzukatu

    Akupempherera

    Ana ake ndi

    Abale onse:

    “Tate, tithandizeni.”

    Zinthu zikamavuta,

    Amakhalabe wolimba,

    N’ngokoma mtima.

    Nyimbo iyi amaikonda:

    (KOLASI)

    ‘N’dzakulimbitsa.

    Usaopetu.

    N’dzakhala nawe.

    N’dzakuthandiza.’

    Ulimbetu mtima.

    Nyimbo yokondedwa:

    “Adzakulimbitsa,

    Adzakuteteza.”

    (VESI LOKOMETSERA)

    Akugwira ntchito

    Sizophwekadi

    Sakudziwa zamawa

    Anzakewatu

    Amamukondadi

    Moti sadandaula

  2. 2. M’lungu amam’patsa mphamvu

    Ndipotu safo’ka.

    Amachita khama kugwira ntchito​—

    Amapemphera mumtima

    Atatopa kwambiri​—

    Mayiyu akuyesetsa.

    Nyimbo ija amaikonda

    Imam’limbikitsa.

    (KOLASI)

    ‘N’dzakulimbitsa.

    Usaopetu.

    N’dzakhala nawe.

    N’dzakuthandiza.’

    Ulimbetu mtima.

    Nyimbo yokondedwa:

    “Adzakulimbitsa,

    Adzakuteteza.”

    “Adzakulimbitsa,

    Adzakuteteza.”