NSANJA YA OLONDA

Tsamba 32

Chichewa
Tsamba 32
/assets/ct/b4d7e1101e/images/syn_placeholder_sqr.png
Tsamba 32

Tsamba 32

▪ Kodi anthu onse abwino amapitadi kumwamba? Onani tsamba 6.

▪ Kodi Mariya analidi “Amayi a Mulungu”? Onani tsamba 8.

▪ Kodi Mulungu amasangalala anthu akamagwiritsa ntchito zithunzi ndi mafano pomulambira? Onani tsamba 9.

▪ N’chiyani chingakuthandizeni ngati mkazi kapena mwamuna wanu ali ndi matenda aakulu kapena anavulala kwambiri? Onani tsamba 10 mpaka 12.

▪ Kodi uthenga wa m’Baibulo unasinthidwa? Onani tsamba 13 ndi 14.

▪ Kodi aliyense m’banja angatani kuti banjalo lizisangalala? Onani tsamba 16 ndi 17.