NSANJA YA OLONDA

Tsamba 32

Chichewa
Tsamba 32
/assets/ct/b4d7e1101e/images/syn_placeholder_sqr.png
Tsamba 32

Tsamba 32

▪ Tchulani zifukwa zinayi zotsimikizira kuti zimene Baibulo limalonjeza n’zoona. Onani tsamba 8.

▪ Kodi muyenera kulankhula motani ndi wachinyamata amene samayankha mafunso anu? Onani tsamba 12.

▪ Kodi makolo angatani kuti aphunzitse ana awo kukhala anthu oyamikira? Onani tsamba 13.

▪ Kodi Yesu ankatchula dzina la Mulungu polalikira Ayuda anzake? Onani tsamba 19.

▪ Kodi n’chiyani chinachititsa kuti munthu wina wa ku Mexico, amene anali m’gulu la zigawenga zotchedwa Ana a Satana, asinthe kwambiri pa moyo wake? Onani tsamba 28.