Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2000

Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2000

Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2000

Zosonyeza deti la kope lopezekamo nkhaniyo

BAIBULO

Buku Labwino? 12/1

Chaka Chabwino Kwambiri Kugaŵira, 1/15

Mauthenga Abwino​—Mbiri Kapena Nthano? 5/15

Mauthenga Obisika? 4/1

MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA

Anadandaula Ndani za Mafuta Amene Yesu Anadzozedwa? 4/15

Angakane Kusudzulidwa, 12/15

Kodi Kunakomera Yehova Kutundudza Kristu? (Yes. 53:10), 8/15

Magazi Ako Omwe, 10/15

Mkwiyo wa Ndani? (Aroma 12:19), 3/15

Zotengedwa M’magazi? 6/15

MBONI ZA YEHOVA

Altiplano ku Peru, 11/15

Anafupidwa Atafufuza kwa Nthaŵi Yaitali (Denmark), 9/1

Buku la Danieli Lifotokozedwa! (Buku la Ulosi wa Danieli), 1/15

Chilumba cha Robinson Crusoe, 6/15

“Chitsanzo cha Mgwirizano,” 10/15

India, 5/15

Italy, 1/15

Kudera Lamapiri la Chiapas (Mexico), 12/15

Kulengeza Ufumu ku Fiji, 9/15

Kumaliza Maphunziro a Gileadi, 6/15, 12/15

Kusodza Anthu ku Nyanja ya Aegean, 4/15

Mamembala Atsopano a Bungwe Lolamulira, 1/1

Matupi Aang’ono, Mitima Yabwino, 2/15

Misonkhano Yachigawo yakuti “Mawu Aulosi a Mulungu,” 1/15

Mtima Wamataya Umadzetsa Chimwemwe (zopereka), 11/1

Poponderezedwa ndi Anazi (Netherlands), 4/1

Senegal, 3/15

Taiwan, 7/15

Tuvalu, 12/15

Ulendo wa ku Zilumba za M’nyanja ya Pacific​—Kuntchito! 8/15

MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU

Abusa Achikristu, ‘Tsegulani Mtima Wanu’! 7/1

Kodi Anthu Achiwawa Mumawaona Monga Momwe Mulungu Amawaonera? 4/15

Kodi Kukhala Mkristu N’chiyani? 6/1

Kodi Kupambana Mumati N’kutani? 11/1

Kodi Mukupindula ndi Zitsanzo Zabwino? 7/1

Kodi Mumadziona Motani? 1/15

Kodi Mumatani Pakakhala Kusamvana? 8/15

Kodi N’chifukwa Chiyani Alibe Ana? 8/1

Kodi Ndinu Mkristu ‘Wokhwima Ndithu’? 8/15

Kodi Ndinu Wozindikira? 10/1

Kudzichepetsa​—Mkhalidwe Umene Umalimbikitsa Mtendere, 3/15

Kufunafuna Yehova ndi Mtima Wokonzekera, 3/1

Kukhala Oganiza Bwino pa Zoyembekeza Zathu, 8/1

Kulemekeza Ulamuliro, 8/1

Kupanga Mzimu Woyera Kukhala Mthandizi Wanga, 10/15

Maukwati Osangalatsa Amene Amalemekeza Yehova, 5/1

Mmene Mungayandikirire kwa Mulungu, 10/15

Mukhoza Kudzisunga M’dziko Lachiwerewereli (Miy. 5), 7/15

Mukudzivomereza Nokha kwa Ena, 4/15

N’chifukwa Chiyani Mumatumikira Mulungu? 12/15

N’kukhaliranji Wodzimana? 9/15

Nyimbo Zomwe Zimakondweretsa Mulungu, 6/1

Pangani Ubwenzi Wathithithi ndi Yehova (Miy. 3), 1/15

Pezani Chitonthozo M’nyonga ya Yehova, 4/15

“Sunga Malangizo Anga, Nukhale ndi Moyo” (Miy. 7), 11/15

“Tchinjiriza Mtima Wako” (Miy. 4), 5/15

Tetezani Dzina Lanu, (Miy. 6), 9/15

Timafunikira Gulu Lolinganizidwa la Yehova, 1/1

Tumikirani Mulungu ndi Mzimu Wofunitsitsa, 11/15

Uphungu Wanzeru wa Mayi (Miy. 31), 2/1

MBIRI YA MOYO WANGA

Anandidalitsa ndi Choloŵa Chapadera (C. Allen), 10/1

Kukumbukira Mlengi Wathu Kuyambira Paunyamata (D. Hibshman), 1/1

Kusafuna Zambiri M’moyo Potumikira Yehova (C. Moyer), 3/1

Kusiya Ntchito Yopanga Zida Kuyamba Ntchito Yopulumutsa Miyoyo (I. Ismailidis), 8/1

Kuthokoza Yehova​—Kupyolera mu Utumiki wa Nthaŵi Zonse! (S. Reynolds), 5/1

Ndinathandizidwa Kuthetsa Manyazi (R. Ulrich), 6/1

“N’takhala ndi Chikhulupiriro Chosafooka”! (H. Müller), 11/1

Nthaŵi Zonse Yehova Amafupa Anthu Ake Okhulupirika V. Duncombe), 9/1

“Simudziŵa Chimene Chidzagwa Maŵa” (H. Jennings), 12/1

Wonyamula Kuunika ku Mayiko Ambiri (G. Young), 7/1

Yehova Ndiye Pothaŵirapo Panga ndi Mphamvu Yanga (M. Filteau), 2/1

NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRA

Akristu Amapeza Chimwemwe Potumikira, 11/15

Chirikizani Chiphunzitso Chaumulungu Molimbika, 5/1

Chiyembekezo cha Chiukiriro N’champhamvu, 7/15

Chiyembekezo cha Chiukiriro N’chotsimikizirika! 7/15

Choloŵa Chathu Chamtengo Wapatali​—Kodi Chimatanthauzanji kwa Inu? 9/1

“Dikirani,” 1/15

Dziko Latsopano​—Kodi Mudzakhalamo? 4/15

‘Dzipulumutseni Nokha Ndi Iwo Akumva Inu,’ 6/1

“Funani Yehova, ndi Mphamvu Yake,” 3/1

Imani Amphumphu ndi Otsimikiza Kotheratu, 12/15

Imvani Chimene Mzimu Unena, 5/1

“Inu Nonse Muli Abale,” 6/15

Khalanibe ndi “Chiyembekezo cha Chipulumutso” Choŵala! 6/1

Khalani ndi Chikhulupiriro M’mawu Aulosi a Mulungu! 5/15

Kodi Atumiki a Mulungu Ndani Lerolino? 11/15

Kodi Muli ndi “Mtima Wa Kristu”? 2/15

Kodi Mwasonkhezeredwa Kukhala Monga Yesu? 2/15

Kodi Oipa Adzakhalabe Kwa Utali Wotani? 2/1

Kodi Zikumbutso za Yehova Mumazikonda Kwambiri? 12/1

Kudzikuza Kumadzetsa Manyazi, 8/1

Kudziŵa “Mtima wa Kristu,” 2/15

Kufesa Mbewu za Choonadi cha Ufumu, 7/1

Kupanga Zinthu Zonse Kukhala Zatsopano​—Monga Kunanenedwera, 4/15

Kupatula Nthaŵi Yoŵerenga ndi Kuphunzira, 10/1

Kuphunzira​—N’kothandiza ndi Kokondweretsa, 10/1

Kusangalala Mwa Mulungu wa Chipulumutso Chathu, 2/1

Kutumikira Limodzi ndi Mlonda, 1/1

Kuŵerenga Baibulo​—N’kopindulitsa ndi Kosangalatsa, 10/1

Labadirani Mawu Aulosi a Mulungu, 4/1

Labadirani Mawu Aulosi a Mulungu a M’tsiku Lathu, 5/15

Lalikani Uthenga Wabwino Mwachangu, 7/1

Lemekezani Anthu Opatsidwa Ulamuliro Pa Inu, 6/15

Lingaliro Laumulungu la Khalidwe Loyera, 11/1

Mmene Yehova Akutitsogolera, 3/15

‘Mulungu, Tumizani Kuunika Kwanu,’ 3/15

Mungakhalebe ndi Khalidwe Loyera, 11/1

Nsembe Zimene Zinakondweretsa Mulungu, 8/15

Nsembe Zotamanda Zimene Zimakondweretsa Yehova, 8/15

“Nthaŵi Yake Siinafike,” 9/15

“Nzeru Ili ndi Odzichepetsa,” 8/1

Omenyana Ndi Mulungu Sadzapambana, 4/1

Sonyezani Mtima wa Kristu, 9/1

Sonyezani Mtima Wodikira! 9/1

Thandizani Ena Kuyenda Moyenera Yehova, 12/15

Ufumu wa Mulungu​—Ulamuliro Watsopano wa Dziko Lapansi, 10/15

“Wamng’ono” Wasanduka “Chikwi,” 1/1

“Yafika Nthaŵi”! 9/15

Yehova Amapereka Mphamvu kwa Wotopa, 12/1

Yehova​—Iye Amene Ali Wolimba Mphamvu, 3/1

Yehova Sadzachedwa, 2/1

Zimene Ufumu wa Mulungu Udzachita, 10/15

“Zinthu Zofunika” Zikudzaza Nyumba ya Yehova, 1/15

NKHANI ZOSIYANASIYANA

“Abale a ku Poland,” 1/1

Antiokeya (Syria), 7/15

Chidani, Kodi chidzatha? 8/15

Chikhulupiriro Chingasinthe Moyo Wanu, 1/1

Chinsinsi cha Chipambano, 2/1

Cyril Lucaris​—Mwamuna Yemwe Anaona Baibulo Kukhala Lofunika, 2/15

Dziko Lopanda Nkhaŵa, 9/15

Kodi Apezanji pa Yezreeli? 3/1

Kodi Malangizo Abwino Mungawapeze Kuti? 6/1

Kodi Muyenera Kufufuza za Zipembedzo Zina? 10/15

Kodi Muyenera Kuwakhulupirira? 12/1

Kodi Mzimu wa Mulungu Umagwira Ntchito Motani Lerolino? 4/1

Kugwira Ntchito “M’munda”​—Nyengo Yotuta Isanafike, 10/15

Kukongola kwa M’kati, 11/15

Kupemphera Kumathandizadi? 11/15

Kuthetsa Ziphuphu, 5/1

‘Kuzungulira Guwa la Nsembe Lanu,’ 5/1

Makhalidwe a M’Baibulo Ndiwo Ali Abwino Koposa, 11/1

Malo Ongoyeserapo Anthu, 10/1

‘Mbuzi ya Kumapiri ya Maonekedwe Osiririka,’ 10/1

Mgwirizano pa Kupembedza Ukuoneka kuti Ungatheke? 12/1

Miyambo ya Khirisimasi​—Kodi Ndi Yachikristu? 12/15

Mmene Mungapezere Mabwenzi, 12/1

Mmene Moyo Wanu Ungakhalire ndi Tanthauzo Lalikulu, 7/15

Moyo Wangwiro Si Loto Chabe! 6/15

Mtendere wa Dziko Lonse Udzakhalapo Motani? 11/1

Mtengo wa Azitona, 5/15

Mulungu Amayankha Mapemphero, 3/1

Mumadziŵa Kudikira? 9/1

Mumakhulupirira Zomwe Simungathe Kuziona? 6/15

Mungapeze Mtendere wa Mumtima, 7/1

Mverani Chenjezo! 2/15

Mwamuna Wachitsanzo Chabwino Amene Anavomera Kum’langiza, (Yobu) 3/15

N’kugonjetseranji Malingaliro Osafuna Kulakwitsa Kanthu? 6/15

“Nthaŵi za Kukonzanso” Zayandikira! 9/1

Osuliza, 7/15

Nyama za M’Baibulo, 2/15

Tingaphunzire ku Banja Loyamba la Anthu, 11/15

Ufiti?, 4/1

Wozunza Aona Kuunika Kwakukulu (Paulo), 1/15

Yosiya, 9/15

OLENGEZA UFUMU AKUSIMBA

2/1, 3/1, 4/1, 5/1, 6/1, 8/1, 9/1, 12/1

YEHOVA

Kodi Yehova Adzakukumbukirani Motani? 2/1

Mulungu Amayankha Mapemphero, 3/1

Wamkulu Kuposa Mitima Yathu, 5/1

YESU KRISTU

Mmene Yesu Kristu Angatithandizire, 3/15