NSANJA YA OLONDA

Tsamba 32

Chichewa
Tsamba 32
/assets/ct/28ada02fb0/images/syn_placeholder_sqr.png
Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi mungachite chiyani kuti mulimbikitse mnzanu amene akudwala kwambiri? ONANI TSAMBA 10-13.

Kodi Hana anali ndani, nanga chikhulupiriro chake chinamuthandiza bwanji kupirira zoipa zimene mkazi mnzake ankamuchitira? ONANI TSAMBA 14-18.

Kodi ndi chinthu chimodzi chiti chimene mungachite kuti mupindule ndi kuwerenga Baibulo? ONANI TSAMBA 19-21.

Kodi Mulungu ali ndi chiyambi? ONANI TSAMBA 28.

Kodi Mulungu amayang’ana chiyani mumtima mwathu? ONANI TSAMBA 29.