NSANJA YA OLONDA

Tsamba 32

Chichewa
Tsamba 32
/assets/ct/28ada02fb0/images/syn_placeholder_sqr.png
Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi anthu analengedwa kuti akakhale kumwamba? ONANI TSAMBA 5.

Kodi tiyenera kuchita chiyani kuti tidzalandire mphotho imene Mulungu adzapereke kwa anthu abwino? ONANI TSAMBA 6.

Kodi Mulungu amafuna kuti Akhristu azisunga Sabata? ONANI TSAMBA 13-15.

Kodi mungawadziwe bwanji anthu amene amalambira Mulungu movomerezeka? ONANI TSAMBA 16-17.

Kodi mungatani ngati apongozi anu amakonda kulowerera za m’banja mwanu? ONANI TSAMBA 26-28.