GALAMUKANI! December 2015 | Kodi N’zotheka Kukhala Ndi Banja Losangalala?

Ngakhale kuti banja lanu ndi lamavuto, mukhoza kumachita zinthu zomwe zingakuthandizeni kuti muzikhala mwamtendere.

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi N’chiyani Chimachititsa Kuti Anthu Azikangana M’banja?

Kodi zimene zafotokokozedwa m’nkhaniyi zinayamba zakuchitikiranipo?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Mungatani Kuti Musamakangane M’banja?

Mfundo 6 zomwe zili m’nkhaniyi zingakuthandizeni kuti musiye kukangana.

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Mungatani Kuti Muzigwirizana Ndi Anthu a M’banja Lanu?

Kodi mukuganiza kuti Baibulo lingakuthandizeni kuti muzikhala mosangalala m’banja? Werengani nkhaniyi kuti muone malangizo othandiza a m’Baibulo.

MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA

Zimene Mungachite Ngati Mumakonda Zosiyana

Kodi mumaona kuti ndinu wosiyana kwambiri ndi mwamuna kapena mkazi wanu?

Kodi Munazionapo Zinsomba Zikuluzikulu Izi?

Kodi nsomba zolemera kwambirizi zimatha bwanji kusambira?

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Imfa

Kodi n’zoona kuti pali chinachake chimene chimapitiriza kukhala ndi moyo munthu akamwalira? Kodi chimachitika n’chiyani munthu akamwalira?

ZOCHITIKA PADZIKOLI

Nkhani za ku Europe

Mungadabwe kuti zotsatira za kafukufuku amene wachitika posachedwapa ku Europe, zikugwirizana kwambiri ndi zimene Baibulo limanena.

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2015

Mitu ya nkhani za mu Galamukani! zomwe zinatuluka m’chaka cha 2015.

KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?

Thupi Lathu Limatha Kudzichiza Lokha

Kodi asayansi akupanga zotani potengera zimene thupi lathu limachita tikavulala?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kupatsa N’kwabwino

Pali zambiri zimene mungachite kuti muthandize ena. Kodi mukuganiza kuti mungachite chiyani?

Wosaona Ndiponso Wosamva

James Ryan anabadwa ndi vuto losamva ndipo kenako anakhalanso ndi vuto losaona. Kodi n’chiyani chinamuthandiza kudziwa cholinga cha moyo?