Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2015 YAMBANI Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2015 CHIPEMBEDZO Kodi Baibulo Ndi Lothandizabe Masiku Ano? 2/15 Kodi Kukhulupirira Zoti Kuli Mulungu N’kothandiza Bwanji? 3/15 Kodi Moyo Unayamba Bwanji? 1/15 Mafunso Atatu Omwe Anthu Amafuna Atafunsa Mulungu, 10/15 N’chifukwa Chiyani Anthu Akusiya Zipembedzo Zawo? 11/15 KUCHEZA NDI ANTHU Katswiri wa Masamu (G. Hwang), 11/15 N’chifukwa Chiyani Wansembe Anasiya Chipembedzo Chake? (A. Della Gatta), 2/15 Sanasiye Kutsatira Zimene Amakhulupirira (S. H. Kang), 8/15 KUCHITA ZINTHU NDI ANTHU Kodi Mukufuna Kubwereranso Kunyumba? 10/15 Kodi Mungatani Kuti Muziugwira Mtima? 1/15 Kodi Mungatani Ngati Chibwenzi Chatha? 7/15 Kodi Mungatani Ngati Mumasowa Wocheza Naye? 4/15 Kodi Mungatani Ngati Kupepesa Kumakuvutani? 9/15 Kodi Mungayankhe Bwanji Mwana Wanu Atakufunsani za Imfa? 2/15 Kodi N’zotheka Kukhala Ndi Banja Losangalala? 12/15 Mungaphunzitse Bwanji Mwana Wanu Kuti Azikumverani? 5/15 Mungatani Kuti Mukwaniritse Lonjezo Lanu? 6/15 Mungatani Kuti Muzigwirizana Ndi Apongozi Anu? 3/15 Musamagwiritse Ntchito Zipangizo Zamakono Monyanyira, 4/15 Muziyamikira Ana Anu, 11/15 N’chifukwa Chiyani Ana a Masiku Ano Safuna Kuuzidwa Zochita? 4/15 Phunzitsani Ana Anu Kuti Akhale Odziletsa 8/15 Zimene Mungachite Ngati Mumakonda Zosiyana, 12/15 MAYIKO NDI ANTHU Costa Rica, 1/15 Honduras, 4/15 Malamulo Omwe Anagawanitsa Dziko, 3/15 Mongolia, 7/15 Nicaragua, 9/15 Uzbekistan, 10/15 MBONI ZA YEHOVA Amaphunzitsa Baibulo Komanso Kuwerenga ndi Kulemba, 8/15 “Mulungu Akutithandiza Kuti Tiiwale Zakale,” 5/15 NYAMA NDI ZOMERA Kodi Munazionapo Nsomba Zikuluzikulu Izi? 12/15 Nsomba Zomwe Zimapanga Mchenga, 6/15 SAYANSI Akadziwotche Omwe Amamva Kwambiri, 3/15 Chisa cha Njuchi, 1/15 Gulo Wakhungu Lodabwitsa Kwambiri, 10/15 Kanyama Kam’madzi Komwe Kamawala Pofuna Kudziteteza, 5/15 Kodi Moyo Unayamba Bwanji? 1/15 Magiya a Kachilombo Kofanana ndi Nyenje, 8/15 Mapiko a Mbalame Opindikira M’mwamba, 2/15 Maselo Athu Ali Ngati Laibulale, 8/15 Nsagwada za Ng’ona, 7/15 Thupi Lathu Limatha Kudzichiza Lokha, 12/15 Tindevu ta Mphaka, 4/15 Tizilombo Tomwe Timachotsa Mafuta, 9/15 Zomera Nazonso Zimadziwa Masamu, 11/15 TIONE ZAKALE Al-Khwarizmi, 5/15 Galileo, 6/15 Herodotus, 9/15 UMOYO NDI MANKHWALA Amachita Zinthu Bwinobwino Ngakhale Kuti Ndi Osaona, 11/15 Kamphepo Kayaziyazi Komanso Dzuwa Ndi Mankhwala, 3/15 Kodi Mungathandize Bwanji Mnzanu Kapena Wachibale Akadwala? 10/15 Malungo, 7/15 ‘Ndimayesetsa Kuti Ndisamangoganizira za Matenda Anga’ (Scleroderma), 1/15 Zimene Mungachite Kuti Mukhale ndi Moyo Wathanzi, 6/15 ZACHUMA NDI NTCHITO Kodi Mungatani Kuti Musakhale Wokonda Ndalama? 9/15 Umphawi Komanso Vuto Losowa Pokhala Zidzatha, 5/15 ZIMENE BAIBULO LIMANENA Chigololo, 6/15 Chiwawa, 5/15 Imfa, 12/15 Kodi Dzikoli Lidzathadi? 11/15 Kodi Zamoyo Zinachita Kusintha Kuchokera ku Zinthu Zina? 10/15 Kukhala Ololera, 8/15 Kutchova Juga, 3/15 Mavuto, 1/15 Mesiya, 2/15 Ntchito, 7/15 Nyama, 4/15 Umphawi, 9/15 ZOSIYANASIYANA Kodi Mumatani Mukakumana ndi Mavuto? 7/15 Nzeru Zomwe Zimateteza, 2/15 Yam'mbuyo Yotsatira