Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kodi Mungayankhe Bwanji?

Kodi Mungayankhe Bwanji?

Kodi Mungayankhe Bwanji?

1. Tchulani maina a atumwi 12.

․․․․․

․․․․․

․․․․․

․․․․․

․․․․․

․․․․․

․․․․․

․․․․․

․․․․․

․․․․․

․․․․․

․․․․․

Lembani mzere wolumikiza dzina la mtumwi ndi zimene ankadziwika kuti ankachita.

2. Analibe chinyengo (Yohane 1:47)

3. Anatchedwa Zelote (Luka 6:15)

4. Anakayikira (Yohane 20:24, 25)

Kambiranani: Kodi ndi mtumwi uti amene mumamukonda kwambiri? Kodi n’chiyani kwenikweni chimakupangitsani kuti muzim’konda?

ZINACHITIKA LITI?

Lembani mzere kuchokera pa chithunzichi kufika pa chaka cholondola.

4216 4026 3375 2370 1593 1513 B.C.E.

5. Eksodo 2:1-7

6. Genesis 2:7

7. Genesis 7:11

NDINE NDANI?

8. Ndinali Mwisrayeli koma sindinali kholo la Mesiya. Mkazi wanga sanali Mwisrayeli koma anali kholo la Mesiya.

NDINE NDANI?

9. Ndinatchedwa “wodalitsika, woposa akazi” chifukwa choti ndinapha mdani wa Israyeli.

KUCHOKERA M’MAGAZINI INO

Yankhani mafunso awa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowekapo.

Tsamba 3 Kodi Yesu ananena kuti chinsinsi chopezera chimwemwe chagona pati? (Mateyu 5:․․․)

Tsamba 5 Kodi Solomo anati chiyani za anthu okonda ndalama? (Mlaliki 5:․․․)

Tsamba 11 Kodi ndi motani mmene Paulo anazunzidwira chifukwa cha chikhulupiriro chake? (2 Akorinto 11:․․․)

Tsamba 28 Kodi Baibulo limapereka chiyembekezo chotani kwa makolo omwe ali ndi ana olumala? (Yesaya 35:․․․)

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungathe kupeza zithunzi izi m’magazini ino? M’mawu anuanu, fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

(Mayankho ali pa tsamba 22)

MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31

1. Simoni, amene ankamutchanso Petro, Andreya mbale wake, Yakobo ndi Yohane, Filipo, Batolomeyo (Natanayeli), Mateyu, Tomasi, Yakobo mwana wa Alifeyo, Simoni wotchedwa Zelote, Yuda mwana wa Yakobo, ndi Yudase Isikariote, amene pambuyo pake anam’pereka.—Luka 6:14-16.

2. Natanayeli.

3. Simoni.

4. Tomasi.

5. Mose—1593 B.C.E.

6. Adamu—4026 B.C.E.

7. Nowa ali m’chingalawa—2370 B.C.E.

8. Maloni.—Rute 4:9, 10.

9. Yaeli.—Oweruza 5:24-27.

[Mawu a Chithunzi patsamba 31]

Bottom circle: Rare Books Division, The New York Public Library, Astor, Lenox and Tilden Foundations