Pitani ku nkhani yake

Mbiri ya Baibulo

Kodi Ndi Ndani Amene Anagawa Machaputala ndi Mavesi a M’Baibulo?

N’chifukwa chiyani anthu ambiri amakonda machaputala ndi mavesi okhala ndi manambala?

Baibulo Linasungidwa Ngakhale Kuti Ena Ankalitsutsa

Atsogoleri andale komanso azipembedzo akhala akuletsa anthu kumasulira, kusindikiza ngakhalenso kukhala ndi Baibulo, koma sizinatheke.

Kodi Tingadziwe Bwanji Kuti Baibulo Limanena Zoona?

Ngati Baibulo linachokeradi kwa Mulungu, ndiye kuti liyenera kukhala losiyana kwambiri ndi mabuku ena onse.

Kodi Baibulo Linasinthidwa Kapena Kusokonezedwa?

Popeza kuti Baibulo ndi buku lakalekale, kodi tingatsimikize bwanji kuti uthenga wake ndi wolondola mpaka pano?

Baibulo Linapulumuka Ngakhale Kuti Ena Ankafuna Kusintha Uthenga Wake

Anthu amaganizo olakwika ankafuna kusintha uthenga wa m’Baibulo. Koma zolinga zawozi zinadziwika ndiponso zinalephereka?