Pitani ku nkhani yake

Omasulira Baibulo

Ankalemekeza Kwambiri Baibulo—Kachigawo ka Vidiyo (William Tyndale)

Umboni wakuti ankakonda kwambiri Baibulo umaonekera mu ntchito imene anagwira imene imatithandizabe masiku ano.

Desiderius Erasmus

Munthu wina ananena kuti Erasmus anali wotchuka mofanana ndi mmene zilili ndi anthu ena amene ndi otchuka padziko lonse masiku ano. Kodi n’chiyani chinam’pangitsa kutchuka chonchi?

Baibulo la Bedell Linathandiza Kuti Anthu Ayambe Kumvetsa Mawu a Mulungu

Baibulo limeneli lakhala likugwiritsidwa ntchito kwa zaka 300.

Elias Hutter Anamasulira Mabaibulo Othandiza Kwambiri

Elias Hutter, yemwe anakhalako m’zaka za m’ma 1500 anamasulira Mabaibulo omwe anali othandiza kwambiri

Lefèvre d’Étaples Ankafuna Kuti Anthu Wamba Adziwe Mawu a Mulungu

Kodi anakwanitsa bwanji kumasulira Baibulo m’Chifulenchi ngakhale kuti ankatsutsidwa?