Pitani ku nkhani yake

Mipukutu ya Baibulo

Dzina la Mulungu Limapezekanso mu Mpukutu Wakale

Onani umboni wosonyeza kuti dzina la Mulungu linkapezeka mu “Chipangano Chatsopano.”

Anapeza Zinthu Zamtengo Wapatali Pamulu wa Zinyalala

Kachidutswa komwe Roberts anapeza ka Uthenga Wabwino wa Yohane, ndiye kachidutswa kakale kwambiri ka Baibulo.

Akwanitsa Kuwerenga Mpukutu Wakale

Mu 1970, asayansi anafukula mpukutu wakupsa ku Ein Gedi m’dziko la Israel ndipo akwanitsa kuona mkati mwake pogwiritsa ntchito njira yamakono yochitira sikani zinthu. Kodi mumpukutuwu mwapezeka zotani?

Baibulo Linasungidwa Bwino Kuti Lisawole

Anthu omwe analemba komanso kukopera Baibulo ankagwiritsa ntchito mipukutu yopangidwa ndi gumbwa komanso zikopa. Kodi zinatheka bwanji kuti mipukutu yambiri ya Baibulo ifike masiku ano?

Kodi Nkhani ya Moyo wa Yesu Imene Ili M’Baibulo Ndi Yolondola?

Dziwani mfundo zokhudza nkhani za m’mabuku a Uthenga Wabwino ndiponso mipukutu yakale kwambiri imene ikudziwika masiku ano.