Malo a Nkhani
Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 4 la 2023
Mu lipotili m’bale wa m’Bungwe Lolamulira akutithandiza kuti tiyembekezere mwachidwi misonkhano ya chigawo ya pamasom’pamaso, akufotokozanso mmene Yehova amatitetezera mwauzimu
Lipoti Lachitatu la Bungwe Lolamulira la 2023
M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza zimene abale athu akuchita posonyeza kuti akupanga Yehova kukhala malo awo othawirapo ngakhale kuti akukumana ndi mavuto.
Lipoti Lachiwiri la Bungwe Lolamulira la 2023
M’bale wa m’Bungwe Lolamulira akupereka lipoti lokhudza abale ndi alongo athu a ku Türkiye komanso akucheza ndi abale awiri.
Lipoti Loyamba la Bungwe Lolamulira la 2023
Tikukulimbikitsani kuti muonere lipotili kuti mumve zilengezo zosangalatsa kwambiri zokhudza ntchito yomanga ya ku Ramapo komanso zokhudza apainiya.