Pitani ku nkhani yake

MAY 26, 2023
NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 4 la 2023

Lipoti la Bungwe Lolamulira la Nambala 4 la 2023

Mu lipotili m’bale wa m’Bungwe Lolamulira akutithandiza kuti tiyembekezere mwachidwi misonkhano ya chigawo ya pamasom’pamaso, akufotokozanso mmene Yehova amatitetezera mwauzimu.