Pitani ku nkhani yake

APRIL 17, 2023
NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti Lachitatu la Bungwe Lolamulira la 2023

Lipoti Lachitatu la Bungwe Lolamulira la 2023

Mu lipotili, m’bale wa m’Bungwe Lolamulira akufotokoza zomwe zachitikira abale athu ku Germany, ku East Africa komanso ku Bahamas. Akufotokozanso zimene abale athuwa akuchita posonyeza kuti akupanga Yehova kukhala malo awo othawirapo.