Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi n’zotheka kuchita zinthu mwachilungamo m’dziko laziphuphuli?

ONANI TSAMBA 5.

Kodi Mawu a Mulungu anathandiza bwanji banja lina lachihindu?

ONANI TSAMBA 9 MPAKA 11.

Kodi tingaphunzire chiyani kwa Rute, yemwe anali mkazi wokhulupirika?

ONANI TSAMBA 19 MPAKA 24.

Kodi n’chiyani chinathandiza munthu wina, yemwe anakula movutika komanso anali chidakwa, kuti akhale ndi banja losangalala?

ONANI TSAMBA 26 NDI 27.