Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kodi Mulungu Amafuna Kuti Anthu Azigwiritsa Ntchito Zizindikiro Pomulambira?

Kodi Mulungu Amafuna Kuti Anthu Azigwiritsa Ntchito Zizindikiro Pomulambira?

Popeza Mulungu sitingamuone, kodi tingakhale naye bwanji pa ubwenzi wabwino? Kodi kugwiritsa ntchito zinthu zooneka pomulambira kungatithandize kukhala naye pa ubwenzi?