NSANJA YA OLONDA March 2015 | Yesu Anatipulumutsa ku Uchimo ndi Imfa

Kodi Yesu amatipulumutsa kwa Satana, ku mkwiyo wa Mulungu kapena ku chiyani?

NKHANI YAPACHIKUTO

N’chifukwa Chiyani Tikufunika Kupulumutsidwa?

Kodi Mulungu wachikondi angalenge anthu ndi mtima wofuna kukhala ndi moyo mpaka kalekale zitakhala kuti zimenezo sizingatheke?

NKHANI YAPACHIKUTO

Yesu Anafa Ndi Kuukitsidwa Kuti Tidzapeze Moyo Wosatha

Mfundo 6 za m’Baibulo zomwe zimafotokoza mmene imfa ya munthu mmodzi ingathandizire kuti anthu ambiri adzapeze moyo wosatha.

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Mwambo Wokumbukira Imfa ya Yesu Udzachitika Liti?

Chaka chino, a Mboni za Yehova adzachita mwambo wokumbukira imfa ya Yesu Lachisanu pa 3 April.

ZIMENE OWERENGA AMAFUNSA

Kodi Akhristu Ayenera Kukondwerera Isitala?

Kodi akatswiri a mbiri yakale amati chiyani za chikondwerero chotchuka chimenechi?

MBIRI YA MOYO WANGA

Jairo Amagwiritsa Ntchito Maso Ake Kutumikira Mulungu

Jairo amadwala matenda a muubongo oopsa kwambiri komabe amaona kuti moyo wake ndi waphindu.

Kodi Mukudziwa?

Kodi kukhala nzika ya Roma kunathandiza bwanji mtumwi Paulo? Kodi kale abusa ankawalipira bwanji?

Mphatso Zoyenera Kupatsa Mfumu

Zonunkhira zomwe masiku ano anthu amatha kuzipeza mosavuta, kale zinali zodula ngati golide.

Kuyankha Mafunso a M’Baibulo

Kodi ndi ndani ayenera kudya mkate komanso vinyo pa mwambo wokumbukira imfa ya Yesu?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Tiyenera Kulambira Mafano?

Kodi Mulungu amasangalala tikamagwiritsa ntchito mafano pomulambira?