NSANJA YA OLONDA March 2013 | Kodi Kuukitsidwa kwa Yesu N’kofunika Bwanji kwa Inu?

Kodi kuuka kwa Yesu kuli ndi phindu lililonse pa moyo wanu?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Yesu Anaukitsidwadi?

Kuuka kwa Yesu ndi chimodzi mwa ziphunzitso zikuluzikulu za m’Baibulo, choncho tifunika kudziwa ngatidi Yesu anaukitsidwa.

NKHANI YAPACHIKUTO

Kuukitsidwa kwa Yesu Kudzapangitsa Anthu Kupeza Moyo Wosatha

Tayerekezani kuti muli m’dziko lopanda mavuto, zopweteka kapena chisoni.

Kodi Mukudziwa?

Kodi Ayuda a m’nthawi ya atumwi ankatsatira mwambo wotani poika maliro? Kodi Yesu anaikidwa m’manda mofanana ndi mmene Ayuda ankaikira maliro?

ZIMENE OWERENGA AMAFUNSA

Kodi Yesu Analonjeza Munthu Wochita Zoipa Kuti Akakhala Naye Kumwamba?

Yesu analonjeza munthu wochita zoipa kuti, ”Udzakhala ndi ine m’Paradaiso.” Kodi pamenepa Yesu ankatanthauza chiyani?

MBIRI YA MOYO WANGA

“Ndinkaona, Koma Sindinkadziwa Tanthauzo Lake”

Olivier anali wogontha ndipo ankakumana ndi mavuto ambirimbiri. Werengani kuti mumve mmene Yehova anamuthandizira.

YANDIKIRANI MULUNGU

“Kodi Lamulo Loyamba Ndi Liti pa Malamulo Onse?”

Zimene Mulungu amafuna tingazinene m’mawu amodzi.

PHUNZITSANI ANA ANU

Petulo ndi Hananiya Ananama, Kodi Tikuphunzirapo Chiyani?

Fufuzani kuti mudziwe chifukwa chake wina anakhululukidwa atanama pomwe wina ayi.

Kuyankha Mafunso a M’Baibulo

N’chifukwa chiyani Baibulo limati Yesu ndi Mwana wa Mulungu? Nanga kodi analengedwa liti?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi a Mboni za Yehova Ndi Akhristu?

Onani chifukwa chake timasiyana ndi zipembedzo zina zimene zimati n’zachikhristu.