NSANJA YA OLONDA

Tsamba 32

Chichewa
Tsamba 32
/assets/ct/fa815d8e9f/images/syn_placeholder_sqr.png
Tsamba 32

Tsamba 32

▪ Ngati muli wokhulupirika kwa Mulungu, kodi iye adzakudalitsani pokupatsani chuma? Onani tsamba 4.

▪ Kodi ndalama n’zimene zimapangitsa munthu kukhala wosangalaladi? Onani tsamba 9.

▪ Kodi pangakhale vuto ngati simukhulupirira kuti Adamu ndi Hava anali anthu enieni? Onani tsamba 12.

▪ Kodi mukuganiza kuti kubwezera n’kwabwino kapena n’koipa? Onani tsamba 20.

▪ Kodi mungapeze chiyani m’nyanja yaikulu ya ku Central America? Onani tsamba 25.