NSANJA YA OLONDA

Tsamba 32

Chichewa
Tsamba 32
/assets/ct/28ada02fb0/images/syn_placeholder_sqr.png
Tsamba 32

Tsamba 32

▪ Kodi dzina la Mulungu ndi ndani? Onani tsamba 6.

▪ Kodi ndani kwenikweni akulamulira dzikoli? Onani tsamba 8.

▪ Ngati muli ndi ana, kodi n’chifukwa chiyani ndi bwino kukhala ndi nthawi yocheza ndi mwamuna kapena mkazi wanu? Onani tsamba 11.

▪ Kodi mayi amene ankazembetsa miyala ya diamondi komanso kuwabera abwana ake anasintha bwanji kukhala woona mtima? Onani masamba 26 ndi 27.

▪ Kodi n’chifukwa chiyani Mboni za Yehova sizigwiritsa ntchito mafano polambira? Onani masamba 30 ndi 31.