NSANJA YA OLONDA

Tsamba 32

Chichewa
Tsamba 32
/assets/ct/79e1b14fff/images/syn_placeholder_sqr.png
Tsamba 32

Tsamba 32

▪ Kodi Baibulo linalosera kale mavuto a masiku anowa? Onani tsamba 6.

▪ Kodi n’zotheka kuti anthufe titsanzire Mulungu? Ngati n’zotheka, kodi tingam’tsanzire motani? Onani tsamba 15.

▪ Kodi bambo amafunika kuti aziwachitira zotani ana ake? Onani tsamba 18.

▪ Kodi tingaphunzire chiyani kwa Mariya poona zimene zinachitika panthawi ya kubadwa kwa Yesu? Onani tsamba 22.

▪ Ngati Adamu anali munthu wangwiro kodi zinatheka bwanji kuti achimwe? Onani tsamba 27.