NSANJA YA OLONDA January 2015 | Kodi Pali Amene Angakhazikitse Boma Lopanda Chinyengo?

Anthu ambiri amaona kuti mabungwe a boma ambiri amachita zinthu zachinyengo. Kodi n’zotheka kukhala ndi boma lopanda chinyengo?

NKHANI YAPACHIKUTO

M’mayiko Ambiri Mukuchitika Zachinyengo

Vutoli ndi lalikulu kwambiri kuposa mmene mungaganizire

NKHANI YAPACHIKUTO

Ufumu wa Mulungu Ndi Boma Lopanda Chinyengo

Mfundo 6 zomwe zingakuthandizeni kudziwa kuti Ufumu wa Mulungu udzathetsa chinyengo chonse.

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

Baibulo Linandithandiza Kupeza Mayankho a Mafunso Anga

Mayli Gündel anasiya kukhulupirira zoti kuli Mulungu bambo ake atamwalira. N’chiyani chinamuthandiza kuyambanso kukhulupirira zoti kuli Mulungu komanso kukhala ndi mtendere wamumtima?

Kodi Amuna Angatani Kuti Akazi Awo Azisangalala?

Amunanu, kodi mumangokwanitsa kupezera banja lanu ndalama, koma n’kulephera kuchitira mkazi wanu zina zofunika kwambiri?

Kodi Mukudziwa?

Kodi mawu achigiriki akuti eu·nouʹkhos amatanthauza chiyani? N’chifukwa chiyani abusa akale ankalekanitsa nkhosa ndi mbuzi?

Kodi Tizipemphera kwa Yesu?

Yesu anatiuza yankho la funso limeneli

Kuyankha Mafunso a M’Baibulo

Kodi anthu analengedwa ndi Mulungu kapena anachokera ku nyama?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani ya Ukwati wa Amuna Kapena Akazi Okhaokha?

Mulungu amene anayambitsa ukwati amadziwa bwino zimene anthu okwatirana angachite kuti akhale ndi banja lolimba komanso losangalala.