NSANJA YA OLONDA June 2013 | Kodi Tsankho Lidzatha Liti?

Mulungu yekha ndi amene angathetseretu tsankho. Komano kodi adzachita bwanji zimenezi ndipo adzazichita liti?

NKHANI YAPACHIKUTO

Tsankho Likuchitika Padziko Lonse

Kodi tsankho n’chiyani? N’chifukwa chiyani tinganene kuti nthawi zina munthu aliyense amapanga zinthu mwatsankho komanso kuti vuto limeneli lili padziko lonse?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Tsankho Lidzatha Liti?

Zitsanzo za anthu ena zimasonyeza kuti Baibulo limathandiza anthu a mitundu yosiyanasiyana kuthana ndi tsankho. Kodi tsankho lidzatha liti?

YANDIKIRANI MULUNGU

Yehova “Alibe Tsankho”

Mulungu amamva mapephero a atumiki ake kaya akhale amtundu uti kapena dziko liti, olemera kaya osauka. Kodi timadziwa bwanji zimenezi?

Chuma chomwe chinabisika kwa zaka zambiri

Werengani kuti mudziwe zimene zinachitika kuti akatswiri apeze Baibulo lakale kwambiri la Chijojiya.

Kodi N’zoyenera Kupemphera kwa Oyera Mtima?

Kuti tipeze yankho la m’Baibulo pa nkhani ya kupemphera kwa oyera mtima, tiyenera kupeza kaye yankho la funso ili: Kodi tiyenera kuopa kupemphera kwa Mulungu?

PHUNZITSANI ANA ANU

Kodi Tingaphunzire Chiyani kwa Munthu Wachifwamba?

Yesu atatsala pang’ono kufa, analonjeza wachifwamba yemwenso anali atatsala pang’ono kufa kuti adzakhala ndi moyo m’Paradaiso. Kodi Yesu ankatanthauza chiyani ndipo Paradaisoyo adzakhala wotani?

Kuyankha Mafunso a M’Baibulo

Ngakhale kuti anthu ayesetsa kuti padzikoli pakhale mtendere, alemphera kubweretsa mtendere padziko lonse. Werengani kuti mudziwe chifukwa chake.

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi a Mboni za Yehova Amalemekeza Zipembedzo Zina?

Dziwani chifukwa chake Akhristu oona amadziwika ndi kulemekeza ena.