NSANJA YA OLONDA May 2012 Kodi Yesu Angayankhe Bwanji Funso Limeneli? Kodi Yesu Ankachita Nawo Ndale? Kodi Akhristu Ayenera Kulowerera Ndale? Kodi Zimene Akhristu Amaphunzitsa Zimathandiza Bwanji Anthu a M’dera Lawo? Kodi Tingakhale Bwanji Mkhristu Weniweni Komanso Nzika Yodalirika? CHINSINSI CHA BANJA LOSANGALALA Zimene Mungachite Kuti Muyambirenso Kukhulupirirana Kodi N’chiyani Chidzachitikire Zipembedzo? Baibulo Limasintha Anthu Kodi Akhristu a M’nthawi ya Atumwi Ankachita Nawo Ndale? Kodi Mukudziwa? Zimene Ndikuphunzira M’Baibulo Kodi Mungatani Kuti Mudzakhale Ndi Tsogolo Labwino? Moyo wa Anthu Akale—Mlimi Amapereka Mphoto kwa Onse Omwe Amamutumikira