NSANJA YA OLONDA January 2012 Kodi Abulahamu Anali Ndani? Abulahamu Anali Munthu Wachikhulupiriro Abulahamu Anali Munthu Wolimba Mtima Abulahamu Anali Munthu Wodzichepetsa Abulahamu Anali Munthu Wachikondi Anthu Ogwirizana Ngakhale Kuti Ali M’mayiko Osiyana Kodi Baibulo Limalosera Zam’tsogolo? “Ine, Yehova Mulungu Wako, Ndagwira Dzanja Lako Lamanja” Baibulo Limasintha Anthu Kodi Mukudziwa? Kodi N’chifukwa Chiyani Mulungu Anauza Abulahamu Kuti Apereke Mwana Wake Nsembe? Anachita Zinthu Mwanzeru, Molimba Mtima Ndiponso Moganizira Ena Pewani Chilichonse Chokhudza Mizimu Yoipa Tsamba 32 Kodi Mungafune Kukuchezerani?