NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) May 2015

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira pa June 29 mpaka pa July 26, 2015.

MBIRI YA MOYO WANGA

Chikondi Changa cha Poyamba Chandithandiza Kupirira

Werengani nkhani ya M’bale Anthony Morris III, yemwe ali mu Bungwe Lolamulira la Mboni za Yehova.

Khalani Maso Satana Akufuna Kukumezani

Tiyenera kusamala kwambiri ndi Satana chifukwa cha makhalidwe ake atatu.

N’zotheka Kugonjetsa Satana

Kodi mungapewe bwanji kunyada, kukonda chuma ndiponso chiwerewere?

Ankaona Malonjezo Ali Patali

Atumiki akale a Mulungu ankaona m’maganizo awo malonjezo a Mulungu.

Tsanzirani Amene Wakulonjezani Moyo Wosatha

Kodi n’zothekadi kumvetsa mavuto amene sitinakumanepo nawo?

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi Gogi wa kudziko la Magogi wotchulidwa m’buku la Ezekieli ndi ndani?

KALE LATHU

Zinthu Zinkayenda Bwino Chifukwa cha Chikondi

Ngati munayamba posachedwa kufika pa misonkhano ya Mboni za Yehova, mwina mungadabwe kudziwa zimene tinkachita kale.