A Mboni za Yehova amapanga mavidiyo amakatuni pofuna kuphunzitsa ana mmene angagwiritsire ntchito mfundo za m’Baibulo. Kodi mavidiyowa amawapanga bwanji? Nanga kodi ana amasangalala akamaonera mavidiyowa? Onerani vidiyoyi kuti mudziwe.