Phunzirani kwa Anzake a Yehova
Phunzirani zambiri kuchokera kwa anthu otchulidwa m’Baibulo omwe anakhala mabwenzi a Yehova!
Yoswa ndi Kalebe
N’chifukwa chiyani Yoswa ndi Kalebe analimba mtima, pamene ena analephera kulimba mtima?
Abigayeli
Kodi Abigayeli anathandiza bwanji mnzake kuti apewe zoipa n’kuchita zabwino?
Abele
Kodi mungaphunzire chiyani kwa Abele pa nkhani yolimbitsa chikhulupiriro chanu?
Hananiya, Misayeli, ndi Azariya
Kodi ungamvere Yehova mofanana ndi anzake aja—Hananiya, Misayeli, ndi Azariya?
Pepani, palibe mawu ofanana ndi omwe mwasankha.