Pitani ku nkhani yake

South Korea

 

2017-07-25

SOUTH KOREA

“Chigamulo cha Khoti Chabwino Kwambiri Chaka Chino”

Khoti la Apilo la Gwangju linagamula kuti anyamata atatu ndi osalakwa pa mlandu womwe ankaimbidwa chifukwa chokana usilikali. Aliyense akuyembekezera kuti khoti lapamwamba kwambiri lipereke chigamulo chake.

2019-10-15

SOUTH KOREA

Akhristu a ku South Korea Anakana Kulowa Usilikali—Nkhani Yosonyeza Chikhulupiriro ndi Kulimba Mtima Kwawo

Kuyambira mu 1953, abale achinyamata a ku Korea akhala akumangidwa chifukwa chokana kulowa usilikali potsatira zomwe amakhulupirira. Koma mu February 2019, zinthu zinasintha. Kodi zinthu zosaiwalikazi zinatheka bwanji?

2018-11-20

SOUTH KOREA

Pamene Chigamulo cha Khoti Lalikulu Kwambiri Chikuyandikira, Wokana Kulowa Usilikali Akuyembekezera Mwachidwi

Pa 30 August, 2018, Khoti Lalikulu Kwambiri ku Korea lidzamva maganizo a anthu pa zimene Khoti Loona za Malamulo linagamula pa mlandu wa anthu okana kulowa usilikali chifukwa cha zimene amakhulupirira.

2018-09-27

SOUTH KOREA

Kuchitira Chilungamo Anthu Okana Usilikali Chifukwa cha Zimene Amakhulupirira ku South Korea: Chigamulo Chomwe Anthu Akhala Akuchiyembekezera kwa Nthawi Yaitali

Popereka chigamulo chake chomwe n’chosaiwalika, Khoti Loona za Malamulo Oyendetsera Dziko linalamula boma la South Korea kuti lilembenso Malamulo a Ntchito ya Usilikali ndipo liphatikizemo mfundo yoti munthu amene sakufuna usilikali azipatsidwa ntchito zina. Khotili linanena kuti boma liyenera kuchita zimenezi pofika kumapeto kwa chaka cha 2019.