NSANJA YA OLONDA May 2014 | Kodi Pali Amene Angadziwiretu za M’tsogolo?

Yankho la funso limeneli lingasinthe moyo wanu.

NKHANI YAPACHIKUTO

Zina Zimachitika, Koma Zambiri Sizichitika

Ndani ali ndi mbiri yoti zimene walosera zimachitikadi?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Pali Amene Angadziwiretu za M’tsogolo?

Baibulo linaneneratu zomwe zidzachitike m’tsogolo.

KUCHEZA NDI MUNTHU WINA

Kodi a Mboni za Yehova Amakhulupirira Yesu?

Ngati amamukhulupirira, n’chifukwa chiyani sanena kuti iwo ndi Mboni za Yesu?

Kodi Mukudziwa?

N’chifukwa chiyani Ayuda anapempha Pilato kuti athyole miyendo ya Yesu? Kodi Davide anaphadi Goliyati ndi gulaye?

TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO

Sanafooke Chifukwa cha Chisoni

Chitsanzo cha Mariya, mayi a Yesu, chingakuthandizeni ngati mukumva chisoni kwambiri chifukwa cha imfa ya munthu wina.

Kuyankha Mafunso a M’Baibulo

Ngati ndi Mulungu amene akulamulira dziko lapansili, n’chifukwa chiyani padzikoli pali mavuto ambiri chonchi?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Baibulo Ndi Lochokera kwa Mulungu?

Anthu ambiri amene analemba Baibulo amati analemba maganizo a Mulungu. N’chifukwa chiyani amatero?