NSANJA YA OLONDA April 2014 | Kodi Kupemphera N’kothandizadi?

Ngati Mulungu amadziwa kale zimene tikufunikira, timafunikadi kupemphera? Baibulo limayankha funso limeneli.

NKHANI YAPACHIKUTO

N’chifukwa Chiyani Anthu Amapemphera kwa Mulungu?

Ngakhale anthu amene sakhulupirira kuti kuli Mulungu, amapemphera. N’chifukwa chiyani?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Kupemphera N’kothandizadi?

Mulungu angayankhe pemphero la munthu popanda kuchita zozizwitsa.

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

Ankagwiritsa Ntchito Baibulo Poyankha Funso Lililonse

Isolina Lamela anali sisitere wakatolika koma anakhumudwa ndi zochita za magulu onse awiri. Kenako anakumana ndi a Mboni za Yehova amene anamuthandiza pogwiritsa ntchito Baibulo kuti adziwe chifukwa chake Mulungu anatilenga.

Mungathe Kukana Mayesero

Pali njira zitatu zimene zingakuthandizeni kulimbana ndi mayesero.

Kodi Mukudziwa?

Kodi kapolo wothawa kwa mbuye wake anali ndi mwayi wotani ku Roma? N’chifukwa chiyani utoto wofiirira wa ku Turo unali wodula kwambiri padziko lonse?

Kodi Thomas Emlyn Ankanyozadi Mulungu Kapena Ankateteza Choonadi?

Zimene anapeza m’Baibulo zinapangitsa kuti tchalitchi komanso anthu ena azidana naye.

Kuyankha Mafunso a M’Baibulo

Yesu adzabweretsa mtendere padziko lapansi.

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Cholinga cha Moyo N’chiyani?

Kodi munayamba mwaganizirapo funso lakuti, ‘Kodi cholinga cha moyo n’chiyani?’ Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Baibulo limanena pa nkhaniyi.