GALAMUKANI! September 2015 | Kodi Mungatani Kuti Musakhale Wokonda Ndalama?

Nkhani za ndalama zingachititse kuti tiziona zinthu molakwika.

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Mungatani Kuti Musakhale Wokonda Ndalama?

M’nkhaniyi muli mafunso 7 amene angakuthandizeni kuti mudzifufuze ngati ndalama mumaziona m’njira yoyenera.

ZOCHITIKA PADZIKOLI

Nkhani za ku Middle East

Zomwe anthu anapeza ku Middle East zimasonyeza kuti nkhani zolembedwa m’Baibulo ndi zoona.

MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA

Kodi Mungatani Ngati Zimakuvutani Kupepesa?

Kodi ndiyenera kupepesabe ngakhale kuti wolakwa si ine?

TIONE ZAKALE

Herodotus

Anali katswiri polemba mbiri chifukwa anachita kafukufuku kwa nthawi yaitali asanalembe buku lake.

ANTHU NDI MAYIKO

Dziko la Nicaragua

nyanja yopanda mchere momwe mumapezeka nsomba za m’nyanja zikuluzikulu monga shaki.

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Umphawi

Kodi anthu osauka kwambiri angakhale osangalala?

KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?

Tizilombo Tomwe Timachotsa Mafuta

Kodi mabakiteriyawa angathandize bwanji kuchotsa mafuta poyerekeza ndi njira zamakono za asayansi

Zina zimene zili pawebusaiti

Uzikhala Wokoma Mtima Ndiponso Wopatsa

Onerani kuti mudziwe mmene Kalebe ndi Sofiya amasangalalira akamagawana zinthu.