GALAMUKANI! August 2015 | M’thupi Lathu Muli Laibulale

Kutulukira za kasanjidwe ka DNA, kwathandiza kuti asayansi atulukire zinthu zina zokhudza zamoyo.

NKHANI YAPACHIKUTO

Maselo Athu Ali Ngati Laibulale

N’chifukwa chiyani asayansi ena anasiya kukhulupirira kuti zamoyo zinachita kusintha?

MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA

Phunzitsani Ana Anu Kuti Akhale Odziletsa

Kupatsa ana anu chilichonse chimene akufuna kungawalepheretse kuphunzira makhalidwe ofunika.

Amaphunzitsa Baibulo Komanso Kuwerenga ndi Kulemba

Mayi wina dzina lake Josefina anayamba kuphunzira kuwerenga ndi kulemba ali ndi zaka 101. Werengani kuti mudziwe zimene zinachitika.

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Kukhala Ololera

Kodi Baibulo limanena kuti tiyenera kukhala ololera mpaka kufika pati?

Sanasiye Kutsatira Zimene Amakhulupirira

Song Hee Kang anakhala wokhulupirika pamene anadwala kwambiri ali ndi zaka 14.

KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?

Magiya a Kachilombo Kofanana ndi Nyenje

Magiyawo amathandiza kachilomboka kuti kazilumpha bwinobwino.

Zina zimene zili pawebusaiti

Muzimvera Makolo Anu

N’chifukwa chiyani kumvera makolo anu kuli kofunika? Onerani vidiyoyi kuti mudziwe chifukwa chake limodzi ndi Kalebe.