GALAMUKANI! May 2015 | Umphawi Komanso Vuto Losowa Pokhala Zidzatha

Baibulo lili ndi mfundo zomwe zingathandize anthu osowa pokhala komanso aumphawi. Limanenanso kuti posachedwapa, Mulungu adzathetseratu umphawi komanso vuto losowa pokhala.

ZOCHITIKA PADZIKOLI

Nkhani za ku Asia

Kodi mayiko a ku Asia akukumana ndi mavuto otani pa nkhani yophunzitsa komanso kuteteza nzika zawo? Kodi mfundo za m’Baibulo zingawathandize?

NKHANI YAPACHIKUTO

Umphawi Komanso Vuto Losowa Pokhala Zidzatha

M’Baibulo muli mfundo zomwe zingathandize anthu omwe akukumana ndi mavuto azachuma kuti asamade nkhawa.

MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA

Mungaphunzitse Bwanji Mwana Wanu Kuti Azikumverani?

Kodi inuyo simugwirizana ndi mwana wanu ndipo nthawi zambiri mumangochita zomwe mwanayo akufuna? M’nkhaniyi muli mfundo 5 zomwe zingathandize makolo kulera bwino ana awo.

“Mulungu Akutithandiza Kuti Tiiwale Zakale”

Anthu atatu omwe anagwidwa ndi zigawenga pa sukulu ina ku Beslan mu 2004 akufotokoza zimene zawathandiza kuiwala zomwe zinawachitikira.

TIONE ZAKALE

Al-Khwarizmi

Anthu amaona kuti Al-Khwarizmi anali katswiri wa masamu chifukwa anayambitsa njira yosovera masamu yomwe ndi yabwino kwambiri.

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Chiwawa

Kodi Mulungu amawaona bwanji anthu ochita zachiwawa? Kodi anthu achiwawa angasinthe

KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?

Kanyama Kam’madzi Komwe Kamawala Pofuna Kudziteteza

Kanyamaka kamawala osati n’cholinga choti kazioneka, koma pofuna kudziteteza.

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani?

Onani mkati mwa Nyumba ya Ufumu kuti mudziwe zimene zimachitika.

Uzipempha Mwaulemu Ndiponso Uzithokoza

Kalebe waphunzira kuti kupempha mwaulemu ndiponso kuthokoza ndi kofunika kwambiri.