GALAMUKANI! March 2013 | Kodi Bambo Wabwino Amatani?

Azibambo ambiri amaona kuti mabanja awo amayenda bwino kwambiri akamatsatira malangizo a m’Baibulo.

Zochitika Padzikoli

Nkhani monga: Kuthetsa njala, kupanikizika ndi ntchito komanso kuipitsa mpweya m’mizinda ya ku China.

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Bambo Wabwino Amatani?

Werengani kuti mudziwe mfundo 5 za m’Baibulo zimene zingakuthandizeni kuti muzikonda ana anu komanso kuti mukhale bambo wabwino.

Mphalapala—Nyama Yakutchire ya Nyanga Zanthambi

Mugoma ndi zimene nyama yaikulu, yochititsa chidwi komanso yamphamvu imeneyi imachita.

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Zolaula

Ngati mukufuna kusangalatsa Mulungu, werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene Mulungu amaonera nkhani yoonera zolaula.

MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA

Khazikitsani Malamulo oti Mwana Wanu Azitsatira

Kodi mungatani ngati mwana wanu wachinyamata sasangalala ndi malamulo amene munakhazikitsa?

TIONE ZAKALE

Robert Boyle

Anali wasayansi komanso ankakhulupira kwambiri Mulungu komanso Baibulo.

KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?

Maso a Kangaude

Kodi kangaude ameneyu amatha bwanji kudziwa kutalika kwa mtunda umene akufuna kudumpha? N’chifukwa chiyani akatswiri akufuna kupanga zinthu potengera kangaudeyu?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Ndingatani Kuti Ndisamachite Zinthu Mozengereza?

Werengani malangizo amene angakuthandizeni kuti musamachite zinthu mozengereza

Loti ndi Banja Lake—Zithunzi Zofotokoza Nkhani

Koperani nkhaniyi kuti mudziwe zimene mungaphunzire pa nkhani yokhudza banja la Loti.