GALAMUKANI! February 2013 | Kodi Osamukira Kudziko Lina Amakapezadi Zimene Akufuna?

Kodi anthu osamukira kudziko lina amakumana ndi mavuto otani?

Zochitika Padzikoli

Werengani nkhaniyi kuti mumve zinthu zochititsa chidwi zochitika m’madera osiyanasiyana padziko lapansi.

MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA

Zimene Mungachite Kuti Musamakangane

Kodi simuchedwa kukangana ndi mwamuna kapena mkazi wanu? Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mfundo zimene zingathandize banja lanu.

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Osamukira Kudziko Lina Amakapezadi Zimene Akufuna?

Kodi mumaona kuti banja lanu likhoza kumasangalala ngati mutasamukira kudziko lina?

KUCHEZA NDI ANTHU

Katswiri Wopanga Maloboti Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake

Massimo Tistarelli akufotokoza chomwe chinamuchititsa kusintha maganizo pa nkhani yoti zamoyo zinachita kusintha.

TIONE ZAKALE

Plato

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake zipembedzo zambiri zachikhristu zinatengera ziphunzitso za Plato.

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Anthu Ovutika

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene Mulungu amathandizira osauka.

KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?

Mchira wa Gulo

Kodi gulo amatha bwanji kudumpha kuchoka pansi kupita pakhoma?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani Zokhudza Mameseji a Pafoni?

Mameseji a pafoni akhoza kuononga ubwenzi wanu ndi anzanu komanso mbiri yanu. Werengani kuti mudziwe mmene zimenezi zingachitikire

Nkhani ya Yakobo ndi Esau

Werengani nkhani ya Yakobo ndi Esau kuti mudziwe zimene anthu apachibalewa anachita kuti ayambenso kugwirizana.