Koperani ndi kusindikiza tsambali. Ndiyeno malizitsani kujambula chithunzichi kenako yankhani mafunsowo pamodzi ndi banja lanu.