Pitani ku nkhani yake

Phunziro 4: Kuba N’koipa

Phunziro 4: Kuba N’koipa

Kalebe akufuna chinthu chomwe si chake. N’chiyani chamuthandiza kuti achite zinthu zoyenera?

Onaninso

ZOCHITA PA GAWO LA KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Kodi Kalebe Akuwerenga Buku Lanji?

Onerani vidiyo yakuti, “Kuba N’koipa.” Kenako sindikizani tsambali ndipo mulikongoletse ndi chekeni.