Ukhale Wofalitsa Wosabatizidwa
Kodi chimafunika ndi chani kuti munthu ukhale wofalitsa wosabatizidwa? Tiyeni tione.
Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi
MAVIDIYO
Phunzirani kwa Anzake a Yehova
Phunzirani zambiri kuchokera kwa anthu otchulidwa m’Baibulo omwe anakhala mabwenzi a Yehova!
ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA
Zoti Ana Achite
Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.