Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Rwanda

 

Mboni za Yehova ku Rwanda

  • Chiwerengero cha Mboni za Yehova—31,541

  • Chiwerengero cha mipingo—562

  • Chiwerengero cha amene anapezeka pamwambo wapachaka wokumbukira imfa ya Khristu—76,441

  • Pa anthu 449 alionse m’dzikoli pali wa Mboni za Yehova m’modzi

  • Chiwerengero cha anthu—13,372,000

2019-08-23

RWANDA

Kukumbukira Nkhondo Yapachiweniweni Yomwe Inachitika ku Rwanda Zaka 25 Zapitazo

Wa Mboni za Yehova ku Rwanda akukumbukira chipwirikiti chomwe chinachitika pa nkhondo yapachiweniweni mu 1994 ndipo akufotokoza mmene chikondi chololera kuvutikira ena chinamupulumutsira.

2016-11-02

RWANDA

Boma la Rwanda Lathetsa Tsankho Limene Limachitika M’masukulu Chifukwa cha Kusiyana kwa Zipembedzo

Zimene boma lachita poteteza ufulu wopembedza umene ana a sukulu ali nawo ndi nkhani yosangalatsa kwambiri kwa ana a sukulu omwe ndi a Mboni.