Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

NYIMBO 9

Yehova Ndi Mfumu

Yehova Ndi Mfumu

(Salimo 97:1)

  1. 1. Tizilemekeza Yehova,

    Ntchito zake zonse n’zachilungamo.

    Tiimbire Mulungu mosangalala,

    Tilalikire ntchito zake.

    (KOLASI)

    Kumwamba ndi dziko zisangalaletu

    Chifukwa Yehova ndi Mfumu.

    Kumwamba ndi dziko zisangalaletu

    Chifukwa Yehova ndi Mfumu.

  2. 2. Lalikira mitundu yonse

    Chifukwa M’lungu atipulumutsa.

    Titamande Yehova Mulungu wathu.

    Tiyenitu timulambire.

    (KOLASI)

    Kumwamba ndi dziko zisangalaletu

    Chifukwa Yehova ndi Mfumu.

    Kumwamba ndi dziko zisangalaletu

    Chifukwa Yehova ndi Mfumu.

  3. 3. Wakhazikitsatu Ufumu,

    Mwana wake ndiye wolamulira.

    Milungu yabodza

    ichite manyazi,

    Tilambire Yehova yekha.

    (KOLASI)

    Kumwamba ndi dziko zisangalaletu

    Chifukwa Yehova ndi Mfumu.

    Kumwamba ndi dziko zisangalaletu

    Chifukwa Yehova ndi Mfumu.